-
Yoswa 8:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Choncho Yoswa ndi amuna onse ankhondo ananyamuka kupita kukamenyana ndi mzinda wa Ai. Yoswa anasankha asilikali amphamvu ndi olimba mtima okwanira 30,000, nʼkuwatumiza usiku.
-