-
Yoswa 8:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Anawalamula kuti: “Inu mukabisale kumbuyo kwa mzindawo. Musakakhale patali kwambiri ndi mzindawo, ndipo nonsenu mukakhale okonzeka.
-