Yoswa 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ine ndi onse amene ndikakhale nawo, tikafika pafupi kwambiri ndi mzindawo. Iwo akakatuluka kuti adzamenyane nafe ngati poyamba paja,+ tikayamba kuthawa.
5 Koma ine ndi onse amene ndikakhale nawo, tikafika pafupi kwambiri ndi mzindawo. Iwo akakatuluka kuti adzamenyane nafe ngati poyamba paja,+ tikayamba kuthawa.