Yoswa 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Akakaona kuti tikuthawa, akatithamangitsa. Tikapitiriza kuthawa kuti tikawatulutse mpaka akafike kutali ndi mzindawo, chifukwa akaganiza kuti, ‘Akuthawa ngati poyamba paja.’+
6 Akakaona kuti tikuthawa, akatithamangitsa. Tikapitiriza kuthawa kuti tikawatulutse mpaka akafike kutali ndi mzindawo, chifukwa akaganiza kuti, ‘Akuthawa ngati poyamba paja.’+