-
Yoswa 8:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Kenako Yoswa anatumiza amunawo ndipo anapita kukabisala. Iwo anakabisala pakati pa Beteli ndi Ai, kumadzulo kwa Ai. Koma usiku umenewo Yoswa anagona limodzi ndi asilikali amene anali nawo.
-