-
Yoswa 8:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Yoswa anadzuka mʼmawa kwambiri nʼkusonkhanitsa asilikaliwo. Atatero ananyamuka ndipo iye limodzi ndi akulu a Isiraeli anatsogolera asilikaliwo ku Ai.
-