Yoswa 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Asilikali onse+ amene anali ndi Yoswa anayenda nʼkukafika pafupi ndi mzindawo, kutsogolo kwake. Atafika anamanga msasa kumpoto kwa Ai, ndipo pakati pa iwo ndi mzindawo panali chigwa.
11 Asilikali onse+ amene anali ndi Yoswa anayenda nʼkukafika pafupi ndi mzindawo, kutsogolo kwake. Atafika anamanga msasa kumpoto kwa Ai, ndipo pakati pa iwo ndi mzindawo panali chigwa.