Yoswa 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho asilikali ambiri anamanga msasa wawo kumpoto kwa mzindawo,+ ndipo ochepa anamanga kumadzulo kwa mzindawo.+ Usikuwo Yoswa ananyamuka nʼkupita pakati pa chigwa chija.
13 Choncho asilikali ambiri anamanga msasa wawo kumpoto kwa mzindawo,+ ndipo ochepa anamanga kumadzulo kwa mzindawo.+ Usikuwo Yoswa ananyamuka nʼkupita pakati pa chigwa chija.