Yoswa 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano Yehova anauza Yoswa kuti: “Loza mzinda wa Ai ndi nthungo* imene ili mʼmanja mwako,+ chifukwa ndiupereka mʼmanja mwako.”+ Choncho Yoswa analoza mzindawo ndi nthungo imene inali mʼmanja mwake.
18 Tsopano Yehova anauza Yoswa kuti: “Loza mzinda wa Ai ndi nthungo* imene ili mʼmanja mwako,+ chifukwa ndiupereka mʼmanja mwako.”+ Choncho Yoswa analoza mzindawo ndi nthungo imene inali mʼmanja mwake.