Yoswa 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Atangouloza, asilikali amene anabisala aja anavumbuluka nʼkuthamangira kumzindawo ndipo anaulanda. Nthawi yomweyo anauyatsa moto.+
19 Atangouloza, asilikali amene anabisala aja anavumbuluka nʼkuthamangira kumzindawo ndipo anaulanda. Nthawi yomweyo anauyatsa moto.+