-
Yoswa 8:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Amuna a ku Ai atatembenuka anangoona utsi uli tolo mumzindawo, ndipo analibiretu mphamvu zoti nʼkuthawira kulikonse. Kenako asilikali a Chiisiraeli amene ankathawira kuchipululu aja, anatembenukira amuna a ku Aiwo.
-