-
Yoswa 8:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Yoswa ndi Aisiraeli onse amene anali naye ataona kuti asilikali omwe anabisala aja alanda mzindawo, ndiponso ataona utsi mumzindawo, anatembenukira amuna a ku Ai nʼkuyamba kuwapha.
-