Yoswa 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno Yoswa anatentha mzinda wa Ai nʼkuusiya uli bwinja loti lidzakhala choncho mpaka kalekale,+ ndipo lilipobe mpaka lero.
28 Ndiyeno Yoswa anatentha mzinda wa Ai nʼkuusiya uli bwinja loti lidzakhala choncho mpaka kalekale,+ ndipo lilipobe mpaka lero.