-
Yoswa 8:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Anamanga guwalo mogwirizana ndi zimene Mose mtumiki wa Yehova analamula Aisiraeli, mogwirizananso ndi zimene zinalembedwa mʼbuku la Chilamulo+ cha Mose kuti: “Guwa lansembe la miyala yathunthu ndiponso yosasema ndi chipangizo chachitsulo.”+ Ndipo iwo anaperekapo kwa Yehova nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano.+
-