Yoswa 8:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Panalibe ngakhale mawu amodzi pa mawu onse amene Mose analamula, amene Yoswa sanawawerenge mokweza pamaso pa mpingo wonse wa Aisiraeli.+ Panalinso akazi ndi ana, komanso alendo+ okhala pakati pawo.+ Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:35 Nsanja ya Olonda,10/1/2000, ptsa. 9-10
35 Panalibe ngakhale mawu amodzi pa mawu onse amene Mose analamula, amene Yoswa sanawawerenge mokweza pamaso pa mpingo wonse wa Aisiraeli.+ Panalinso akazi ndi ana, komanso alendo+ okhala pakati pawo.+