Yoswa 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamene tinkanyamuka kubwera kuno, mkate wathuwu unali wotentha. Koma mutha kuona kuti wauma ndipo ukungoyoyoka.+
12 Pamene tinkanyamuka kubwera kuno, mkate wathuwu unali wotentha. Koma mutha kuona kuti wauma ndipo ukungoyoyoka.+