Yoswa 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma Aisiraeli sanawaphe anthuwo chifukwa atsogoleri awo anali atalumbirira anthuwo mʼdzina la Yehova,+ Mulungu wa Isiraeli. Choncho gulu lonse linayamba kungʼungʼudza motsutsana ndi atsogoleriwo.
18 Koma Aisiraeli sanawaphe anthuwo chifukwa atsogoleri awo anali atalumbirira anthuwo mʼdzina la Yehova,+ Mulungu wa Isiraeli. Choncho gulu lonse linayamba kungʼungʼudza motsutsana ndi atsogoleriwo.