Yoswa 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako Yoswa anaitana anthuwo nʼkuwafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani munatipusitsa nʼkumanena kuti ‘Timakhala kutali kwambiri ndi inu,’ chonsecho mumakhala pafupi?+
22 Kenako Yoswa anaitana anthuwo nʼkuwafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani munatipusitsa nʼkumanena kuti ‘Timakhala kutali kwambiri ndi inu,’ chonsecho mumakhala pafupi?+