Yoswa 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 anachita mantha kwambiri+ chifukwa Gibiyoni unali mzinda waukulu ngati mzinda wolamulidwa ndi mfumu. Komanso mzindawo unali waukulu kuposa mzinda wa Ai,+ ndipo amuna onse akumeneko anali asilikali.
2 anachita mantha kwambiri+ chifukwa Gibiyoni unali mzinda waukulu ngati mzinda wolamulidwa ndi mfumu. Komanso mzindawo unali waukulu kuposa mzinda wa Ai,+ ndipo amuna onse akumeneko anali asilikali.