Yoswa 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho Yoswa ananyamuka ku Giligala limodzi ndi amuna onse ankhondo ndiponso asilikali amphamvu.+