Yoswa 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Palibe tsiku ngati limeneli, kaya pambuyo pake kapena patsogolo pake, limene Yehova anamvera mawu a munthu mʼnjira imeneyi,+ popeza Yehova anamenyera nkhondo Isiraeli.+
14 Palibe tsiku ngati limeneli, kaya pambuyo pake kapena patsogolo pake, limene Yehova anamvera mawu a munthu mʼnjira imeneyi,+ popeza Yehova anamenyera nkhondo Isiraeli.+