Yoswa 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma enanu musangoima. Thamangitsani adani anu ndipo mukapeza aliyense muzimupha.+ Musawalole kuti akalowe mʼmizinda yawo, chifukwa Yehova Mulungu wanu wawapereka mʼmanja mwanu.”
19 Koma enanu musangoima. Thamangitsani adani anu ndipo mukapeza aliyense muzimupha.+ Musawalole kuti akalowe mʼmizinda yawo, chifukwa Yehova Mulungu wanu wawapereka mʼmanja mwanu.”