Yoswa 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atapita nawo kwa Yoswa, iye anaitana amuna onse a Isiraeli amene anapita naye kunkhondoko nʼkuuza atsogoleri awo kuti: “Bwerani apa muponde kumbuyo kwa makosi a mafumuwa.” Iwo anapita nʼkupondadi kumbuyo kwa makosi a mafumuwo.+
24 Atapita nawo kwa Yoswa, iye anaitana amuna onse a Isiraeli amene anapita naye kunkhondoko nʼkuuza atsogoleri awo kuti: “Bwerani apa muponde kumbuyo kwa makosi a mafumuwa.” Iwo anapita nʼkupondadi kumbuyo kwa makosi a mafumuwo.+