Yoswa 10:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kenako Yoswa ndi Aisiraeli onse anachoka ku Lakisi nʼkupita ku Egiloni.+ Kumeneko anamanga msasa nʼkuyamba kumenyana ndi anthu amumzindawo.
34 Kenako Yoswa ndi Aisiraeli onse anachoka ku Lakisi nʼkupita ku Egiloni.+ Kumeneko anamanga msasa nʼkuyamba kumenyana ndi anthu amumzindawo.