Yoswa 10:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Analanda mzindawo tsiku lomwelo nʼkupha ndi lupanga anthu onse mumzindawo ngati mmene anachitira ku Lakisi.+
35 Analanda mzindawo tsiku lomwelo nʼkupha ndi lupanga anthu onse mumzindawo ngati mmene anachitira ku Lakisi.+