Yoswa 10:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Yoswa anagonjetsa mafumu onsewa nʼkulanda malo awo pa nthawi imodzi, chifukwa Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi amene ankawamenyera nkhondo.+
42 Yoswa anagonjetsa mafumu onsewa nʼkulanda malo awo pa nthawi imodzi, chifukwa Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi amene ankawamenyera nkhondo.+