-
Yoswa 11:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Mafumu onsewa anagwirizana kuti akumane pamodzi, ndipo anakamanga msasa pafupi ndi madzi a ku Meromu kuti amenyane ndi Aisiraeli.
-