Yoswa 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Aisiraeliwo anapha ndi lupanga munthu aliyense amene anali mumzindawo. Panalibe chamoyo chilichonse chimene chinatsala,+ ndipo Yoswa anatentha mzinda wa Hazori. Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:11 Galamukani!,5/2012, tsa. 18
11 Aisiraeliwo anapha ndi lupanga munthu aliyense amene anali mumzindawo. Panalibe chamoyo chilichonse chimene chinatsala,+ ndipo Yoswa anatentha mzinda wa Hazori.