Yoswa 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Fuko la Levi lokha ndi limene sanalipatse malo monga cholowa chawo.+ Cholowa chawo ndi nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ mogwirizana ndi zimene anawalonjeza.+
14 Fuko la Levi lokha ndi limene sanalipatse malo monga cholowa chawo.+ Cholowa chawo ndi nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ mogwirizana ndi zimene anawalonjeza.+