-
Yoswa 13:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Dera limeneli linali cholowa cha anthu a fuko la Gadi chimene anapatsidwa motsatira mabanja awo. Iwo anapatsidwa derali limodzi ndi mizinda komanso midzi ya kumeneko.
-