Yoswa 13:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Chimenechi ndi cholowa chimene Mose anawapatsa kuti chikhale chawo, pamene anali mʼchipululu cha Mowabu, kutsidya kwa mtsinje wa Yorodano, chakumʼmawa kwa Yeriko.+
32 Chimenechi ndi cholowa chimene Mose anawapatsa kuti chikhale chawo, pamene anali mʼchipululu cha Mowabu, kutsidya kwa mtsinje wa Yorodano, chakumʼmawa kwa Yeriko.+