Yoswa 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova wandisunga ndi moyo+ mogwirizana ndi zimene analonjeza.+ Tsopano padutsa zaka 45 kuchokera pamene Yehova analonjeza Mose pa nthawi imene Aisiraeli anali mʼchipululu.+ Lero ndili ndi zaka 85.
10 Yehova wandisunga ndi moyo+ mogwirizana ndi zimene analonjeza.+ Tsopano padutsa zaka 45 kuchokera pamene Yehova analonjeza Mose pa nthawi imene Aisiraeli anali mʼchipululu.+ Lero ndili ndi zaka 85.