-
Yoswa 14:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndipo ndine wamphamvu ngati mmene ndinalili tsiku limene Mose anandituma. Mphamvu zanga zidakali mmene zinalili pa nthawiyo, moti ndikhoza kupita kunkhondo komanso kuchita zinthu zina.
-