Yoswa 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Malire akumʼmawa anali Nyanja Yamchere* mpaka pamene mtsinje wa Yorodano umathira mʼnyanjayi. Malire akumpoto anakhota pagombe pamene mtsinje wa Yorodano umathirira mʼnyanjayi.+
5 Malire akumʼmawa anali Nyanja Yamchere* mpaka pamene mtsinje wa Yorodano umathira mʼnyanjayi. Malire akumpoto anakhota pagombe pamene mtsinje wa Yorodano umathirira mʼnyanjayi.+