Yoswa 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuchokera pamwamba pa phirilo, malirewo anakafika kukasupe wa madzi a Nafitoa,+ nʼkupitirira mpaka kumizinda ya mʼmbali mwa phiri la Efuroni. Anapitirirabe mpaka ku Baala, kutanthauza Kiriyati-yearimu.+
9 Kuchokera pamwamba pa phirilo, malirewo anakafika kukasupe wa madzi a Nafitoa,+ nʼkupitirira mpaka kumizinda ya mʼmbali mwa phiri la Efuroni. Anapitirirabe mpaka ku Baala, kutanthauza Kiriyati-yearimu.+