Yoswa 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene Akisa ankapita kunyumba, anauza Otiniyeli kuti apemphe munda kwa Kalebe bambo ake. Kenako Akisa anatsika pabulu.* Atatero Kalebe anamʼfunsa kuti: “Ukufuna chiyani?”+
18 Pamene Akisa ankapita kunyumba, anauza Otiniyeli kuti apemphe munda kwa Kalebe bambo ake. Kenako Akisa anatsika pabulu.* Atatero Kalebe anamʼfunsa kuti: “Ukufuna chiyani?”+