Yoswa 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kuchokera ku Tapuwa,+ malirewo analowera chakumadzulo kuchigwa cha Kana nʼkukathera kunyanja.+ Chimenechi ndi cholowa cha fuko la Efuraimu motsatira mabanja awo.
8 Kuchokera ku Tapuwa,+ malirewo analowera chakumadzulo kuchigwa cha Kana nʼkukathera kunyanja.+ Chimenechi ndi cholowa cha fuko la Efuraimu motsatira mabanja awo.