Yoswa 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Cholowa cha ana a Efuraimu chinaphatikizapo mizinda imene inali mkati mwa cholowa cha Manase,+ mizinda yonse ndi midzi yake.
9 Cholowa cha ana a Efuraimu chinaphatikizapo mizinda imene inali mkati mwa cholowa cha Manase,+ mizinda yonse ndi midzi yake.