Yoswa 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Malire a gawolo anatsetserekera kuchigwa cha Kana kenako analowera kumʼmwera kwa chigwachi. Pakati pa mizinda ya Manase panali mizinda ya Efuraimu+ ndipo malire a fuko la Manasewo anali kumpoto kwa chigwachi, ndipo anakathera kunyanja.+
9 Malire a gawolo anatsetserekera kuchigwa cha Kana kenako analowera kumʼmwera kwa chigwachi. Pakati pa mizinda ya Manase panali mizinda ya Efuraimu+ ndipo malire a fuko la Manasewo anali kumpoto kwa chigwachi, ndipo anakathera kunyanja.+