Yoswa 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 koma mutengenso dera lamapiri.+ Ngakhale kuti ndi lankhalango, mudzagwetsamo mitengo ndipo gawo lanu likathera kumeneko. Mudzathamangitsa Akanani ngakhale kuti ndi amphamvu ndipo ali ndi magaleta ankhondo okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa.”+
18 koma mutengenso dera lamapiri.+ Ngakhale kuti ndi lankhalango, mudzagwetsamo mitengo ndipo gawo lanu likathera kumeneko. Mudzathamangitsa Akanani ngakhale kuti ndi amphamvu ndipo ali ndi magaleta ankhondo okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa.”+