Yoswa 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho Yoswa anafunsa Aisiraeli kuti: “Kodi muzengereza mpaka liti osapita kukalanda dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu wakupatsani?+
3 Choncho Yoswa anafunsa Aisiraeli kuti: “Kodi muzengereza mpaka liti osapita kukalanda dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu wakupatsani?+