-
Yoswa 18:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Sankhani amuna atatu pa fuko lililonse oti ndiwatume. Akayendere dzikolo nʼkulemba mmene lilili kuti lidzagawidwe mogwirizana ndi cholowa cha mafuko awo. Akatero adzabwerere kwa ine.
-