Yoswa 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno adzagawe dzikolo mʼzigawo 7.+ Fuko la Yuda lidzakhalabe kugawo lawo kumʼmwera,+ ndipo a mʼbanja la Yosefe adzakhalabe kugawo lawo kumpoto.+
5 Ndiyeno adzagawe dzikolo mʼzigawo 7.+ Fuko la Yuda lidzakhalabe kugawo lawo kumʼmwera,+ ndipo a mʼbanja la Yosefe adzakhalabe kugawo lawo kumpoto.+