-
Yoswa 18:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Amunawo anapitadi kukayendera dzikolo ndipo analigawa mʼzigawo 7 potsatira mizinda yake nʼkulemba mʼbuku. Atamaliza anabwerera kwa Yoswa kumsasa ku Silo.
-