Yoswa 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Zela,+ Ha-elefi, Yebusi, kutanthauza Yerusalemu,+ Gibea+ ndi Kiriyati. Mizinda 14 ndi midzi yake. Chimenechi chinali cholowa cha ana a Benjamini motsatira mabanja awo. Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:28 Mawu a Mulungu, ptsa. 95-96
28 Zela,+ Ha-elefi, Yebusi, kutanthauza Yerusalemu,+ Gibea+ ndi Kiriyati. Mizinda 14 ndi midzi yake. Chimenechi chinali cholowa cha ana a Benjamini motsatira mabanja awo.