Yoswa 19:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ichi chinali cholowa cha fuko la Aseri motsatira mabanja awo+ ndipo imeneyi inali mizinda yawo ndi midzi yake.
31 Ichi chinali cholowa cha fuko la Aseri motsatira mabanja awo+ ndipo imeneyi inali mizinda yawo ndi midzi yake.