-
Yoswa 19:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Malirewo anabwerera kumadzulo ku Azinotu-tabori, nʼkupitirira mpaka ku Hukoku nʼkukafika ku Zebuloni kumʼmwera. Anakafikanso ku Aseri kumadzulo ndi ku Yuda chakumʼmawa, kumtsinje wa Yorodano.
-