Yoswa 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu a mʼbanja la Merari+ anapatsidwa mizinda 12 yochokera mʼfuko la Rubeni, la Gadi ndi la Zebuloni,+ motsatira mabanja awo.
7 Anthu a mʼbanja la Merari+ anapatsidwa mizinda 12 yochokera mʼfuko la Rubeni, la Gadi ndi la Zebuloni,+ motsatira mabanja awo.