Yoswa 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mizinda yonse imene anapereka kwa ansembe, ana a Aroni, inalipo 13 ndi malo ake odyetserako ziweto.+
19 Mizinda yonse imene anapereka kwa ansembe, ana a Aroni, inalipo 13 ndi malo ake odyetserako ziweto.+