-
Yoswa 21:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Mabanja a ana a Kohati, kapena kuti Alevi otsala, anapatsidwa mizinda yochokera mʼfuko la Efuraimu pambuyo pochita maere.
-